Quran with Chichewa translation - Surah An-Nahl ayat 13 - النَّحل - Page - Juz 14
﴿وَمَا ذَرَأَ لَكُمۡ فِي ٱلۡأَرۡضِ مُخۡتَلِفًا أَلۡوَٰنُهُۥٓۚ إِنَّ فِي ذَٰلِكَ لَأٓيَةٗ لِّقَوۡمٖ يَذَّكَّرُونَ ﴾
[النَّحل: 13]
﴿وما ذرأ لكم في الأرض مختلفا ألوانه إن في ذلك لآية لقوم﴾ [النَّحل: 13]
Khaled Ibrahim Betala “Ndiponso ndi zimene adakulengerani m’nthaka (zinthu zododornetsa monga nyama, mmera, miyala yamtengo wapatali, zamoyo ndi zopanda moyo), zautoto wosiyanasiyana ndi maonekedwe osiyanasiyana; ndithu m’zimenezo muli zisonyezo kwa anthu olalikika |