×

Ndipo patsiku limene Ife tidzadzutsa mboni kuchokerakumtunduuliwonse, iwoamenesanakhulupirire sadzapatsidwa mwayi 16:84 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nahl ⮕ (16:84) ayat 84 in Chichewa

16:84 Surah An-Nahl ayat 84 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nahl ayat 84 - النَّحل - Page - Juz 14

﴿وَيَوۡمَ نَبۡعَثُ مِن كُلِّ أُمَّةٖ شَهِيدٗا ثُمَّ لَا يُؤۡذَنُ لِلَّذِينَ كَفَرُواْ وَلَا هُمۡ يُسۡتَعۡتَبُونَ ﴾
[النَّحل: 84]

Ndipo patsiku limene Ife tidzadzutsa mboni kuchokerakumtunduuliwonse, iwoamenesanakhulupirire sadzapatsidwa mwayi

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ويوم نبعث من كل أمة شهيدا ثم لا يؤذن للذين كفروا ولا, باللغة نيانجا

﴿ويوم نبعث من كل أمة شهيدا ثم لا يؤذن للذين كفروا ولا﴾ [النَّحل: 84]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo (akumbutse za) tsiku lomwe tidzautsa mboni mu mtundu uliwonse; kenako sikudzaloledwa, kwa amene sadakhulupirire, (kupereka madandaulo) ndipo iwo sadzauzidwa kuti afunefune chiyanjo cha Allah (koma chilango basi)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek