×

Zinthuzimenezilindiinundizakuthakomazimenezili kwa Mulungu ndi zosatha. Ndithudi Ife tidzalipira anthu omwe amapirira malipiro 16:96 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nahl ⮕ (16:96) ayat 96 in Chichewa

16:96 Surah An-Nahl ayat 96 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nahl ayat 96 - النَّحل - Page - Juz 14

﴿مَا عِندَكُمۡ يَنفَدُ وَمَا عِندَ ٱللَّهِ بَاقٖۗ وَلَنَجۡزِيَنَّ ٱلَّذِينَ صَبَرُوٓاْ أَجۡرَهُم بِأَحۡسَنِ مَا كَانُواْ يَعۡمَلُونَ ﴾
[النَّحل: 96]

Zinthuzimenezilindiinundizakuthakomazimenezili kwa Mulungu ndi zosatha. Ndithudi Ife tidzalipira anthu omwe amapirira malipiro abwino kwambiri molingana ndi zimene anali kuchita

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ما عندكم ينفد وما عند الله باق ولنجزين الذين صبروا أجرهم بأحسن, باللغة نيانجا

﴿ما عندكم ينفد وما عند الله باق ولنجزين الذين صبروا أجرهم بأحسن﴾ [النَّحل: 96]

Khaled Ibrahim Betala
“Zomwe mulinazo nzakutha ndipo zili kwa Allah ndizo zosatha. Ndithudi Ife tidzawapatsa malipiro (aakulu zedi) amene adapirira oposera zabwino zimene ankachita
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek