×

Ifetavumbulutsa Bukula Koranim’choonadindipondi m’choonadi latsika. Ndipo Ife takutumiza iwe osati wina kuti 17:105 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Isra’ ⮕ (17:105) ayat 105 in Chichewa

17:105 Surah Al-Isra’ ayat 105 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Isra’ ayat 105 - الإسرَاء - Page - Juz 15

﴿وَبِٱلۡحَقِّ أَنزَلۡنَٰهُ وَبِٱلۡحَقِّ نَزَلَۗ وَمَآ أَرۡسَلۡنَٰكَ إِلَّا مُبَشِّرٗا وَنَذِيرٗا ﴾
[الإسرَاء: 105]

Ifetavumbulutsa Bukula Koranim’choonadindipondi m’choonadi latsika. Ndipo Ife takutumiza iwe osati wina kuti ukalalikire nkhani za bwino ndi kupereka chenjezo

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وبالحق أنـزلناه وبالحق نـزل وما أرسلناك إلا مبشرا ونذيرا, باللغة نيانجا

﴿وبالحق أنـزلناه وبالحق نـزل وما أرسلناك إلا مبشرا ونذيرا﴾ [الإسرَاء: 105]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo chifukwa chobweretsa choonadi pa dziko tidaitumiza (Qur’an); ndipo mwachoonadi, yavumbulutsidwa. Ndipo sitidakutume (ndi china) koma kuti ukhale wouza (okhulupirira) nkhani zabwino, ndi wochenjeza (osakhulupirira)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek