×

Ndipo pambuyo pake Ife tidati kwa ana a Israyeli, “Khalani m’dziko ndipo 17:104 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Isra’ ⮕ (17:104) ayat 104 in Chichewa

17:104 Surah Al-Isra’ ayat 104 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Isra’ ayat 104 - الإسرَاء - Page - Juz 15

﴿وَقُلۡنَا مِنۢ بَعۡدِهِۦ لِبَنِيٓ إِسۡرَٰٓءِيلَ ٱسۡكُنُواْ ٱلۡأَرۡضَ فَإِذَا جَآءَ وَعۡدُ ٱلۡأٓخِرَةِ جِئۡنَا بِكُمۡ لَفِيفٗا ﴾
[الإسرَاء: 104]

Ndipo pambuyo pake Ife tidati kwa ana a Israyeli, “Khalani m’dziko ndipo pamene lonjezo lomaliza lidzadza, Ife tidzakusonkhanitsani kukhala malo amodzi.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وقلنا من بعده لبني إسرائيل اسكنوا الأرض فإذا جاء وعد الآخرة جئنا, باللغة نيانجا

﴿وقلنا من بعده لبني إسرائيل اسكنوا الأرض فإذا جاء وعد الآخرة جئنا﴾ [الإسرَاء: 104]

Khaled Ibrahim Betala
“(Mûsa ndi anthu ake tidawapulumutsa). Ndipo tidati, kwa ana a Israyeli, pambuyo pake (pommiza Farawo): “Khalani m’dziko (loyera la Shami); ndipo likazadza lonjezo la moyo winawo, tidzakubweretsani nonsenu (muli m’chipwirikiti.)”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek