Quran with Chichewa translation - Surah Al-Isra’ ayat 14 - الإسرَاء - Page - Juz 15
﴿ٱقۡرَأۡ كِتَٰبَكَ كَفَىٰ بِنَفۡسِكَ ٱلۡيَوۡمَ عَلَيۡكَ حَسِيبٗا ﴾
[الإسرَاء: 14]
﴿اقرأ كتابك كفى بنفسك اليوم عليك حسيبا﴾ [الإسرَاء: 14]
Khaled Ibrahim Betala “(Kudzanenedwa kwa iye:) “Werenga kaundula wako (kupyolera m’mphamvu za Allah ngakhale pa dziko lapansi siunkatha kuwerenga); mzimu wako ukwanira lero kudziwerengera.” |