×

Aliyense amene achita zabwino atero podzipulumutsa yekha. Ndipo aliyense amene achita zoipa, 17:15 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Isra’ ⮕ (17:15) ayat 15 in Chichewa

17:15 Surah Al-Isra’ ayat 15 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Isra’ ayat 15 - الإسرَاء - Page - Juz 15

﴿مَّنِ ٱهۡتَدَىٰ فَإِنَّمَا يَهۡتَدِي لِنَفۡسِهِۦۖ وَمَن ضَلَّ فَإِنَّمَا يَضِلُّ عَلَيۡهَاۚ وَلَا تَزِرُ وَازِرَةٞ وِزۡرَ أُخۡرَىٰۗ وَمَا كُنَّا مُعَذِّبِينَ حَتَّىٰ نَبۡعَثَ رَسُولٗا ﴾
[الإسرَاء: 15]

Aliyense amene achita zabwino atero podzipulumutsa yekha. Ndipo aliyense amene achita zoipa, atero podzipweteka yekha. Palibe amene adzanyamula katundu wa mnzake. Ndipo Ife sitilanga pokhapokha ngati tatumiza Mtumwi

❮ Previous Next ❯

ترجمة: من اهتدى فإنما يهتدي لنفسه ومن ضل فإنما يضل عليها ولا تزر, باللغة نيانجا

﴿من اهتدى فإنما يهتدي لنفسه ومن ضل فإنما يضل عليها ولا تزر﴾ [الإسرَاء: 15]

Khaled Ibrahim Betala
“Amene waongoka (potsatira njira ya choonadi) ndithu wadzipindulira yekha, ndipo amene wapotoka (ku njira ya choonadi) ndithu wadzitaya iye mwini. Ndipo msenzi wosenza machimo sadzasenza mtolo wa machimo a wina. Ndipo Ife siolanga (zolengedwa) kufikira titatumiza mtumiki (kuti azidziwitse choonadi. Zikakana ndipomwe timazilanga)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek