×

Ndipo yense amene afuna moyo umene uli nkudza, ndi kumaugwirira ntchito zake 17:19 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Isra’ ⮕ (17:19) ayat 19 in Chichewa

17:19 Surah Al-Isra’ ayat 19 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Isra’ ayat 19 - الإسرَاء - Page - Juz 15

﴿وَمَنۡ أَرَادَ ٱلۡأٓخِرَةَ وَسَعَىٰ لَهَا سَعۡيَهَا وَهُوَ مُؤۡمِنٞ فَأُوْلَٰٓئِكَ كَانَ سَعۡيُهُم مَّشۡكُورٗا ﴾
[الإسرَاء: 19]

Ndipo yense amene afuna moyo umene uli nkudza, ndi kumaugwirira ntchito zake molimbika, ndipo ndi wokhulupirira, amenewo ndi amene ntchito zawo zidzakhala zoyamikidwa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ومن أراد الآخرة وسعى لها سعيها وهو مؤمن فأولئك كان سعيهم مشكورا, باللغة نيانجا

﴿ومن أراد الآخرة وسعى لها سعيها وهو مؤمن فأولئك كان سعيهم مشكورا﴾ [الإسرَاء: 19]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo amene afuna tsiku la chimaliziro (mzochita zake) ndikuligwilira ntchito yake yeniyeni uku ali okhulupirira, iwowo khama lawo lidzakhala lolandiridwa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek