×

Ndipo apatseni abale anu ndi anthu ovutika gawo lawo lowayenera ndiponso a 17:26 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Isra’ ⮕ (17:26) ayat 26 in Chichewa

17:26 Surah Al-Isra’ ayat 26 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Isra’ ayat 26 - الإسرَاء - Page - Juz 15

﴿وَءَاتِ ذَا ٱلۡقُرۡبَىٰ حَقَّهُۥ وَٱلۡمِسۡكِينَ وَٱبۡنَ ٱلسَّبِيلِ وَلَا تُبَذِّرۡ تَبۡذِيرًا ﴾
[الإسرَاء: 26]

Ndipo apatseni abale anu ndi anthu ovutika gawo lawo lowayenera ndiponso a paulendo amene avutika. Ndipo musapereke chuma chanu moononga

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وآت ذا القربى حقه والمسكين وابن السبيل ولا تبذر تبذيرا, باللغة نيانجا

﴿وآت ذا القربى حقه والمسكين وابن السبيل ولا تبذر تبذيرا﴾ [الإسرَاء: 26]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo mnansi wako, masikini ndi wapaulendo (yemwe alibe choyendera) mpatse gawo lake (la chuma chako) ndipo usamwaze (chuma chako) mosakaza
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek