×

Ndithudi Ife tafotokoza chinthu chilichonse m’Korani iyi kuti iwo achenjezedwe, koma iyo 17:41 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Isra’ ⮕ (17:41) ayat 41 in Chichewa

17:41 Surah Al-Isra’ ayat 41 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Isra’ ayat 41 - الإسرَاء - Page - Juz 15

﴿وَلَقَدۡ صَرَّفۡنَا فِي هَٰذَا ٱلۡقُرۡءَانِ لِيَذَّكَّرُواْ وَمَا يَزِيدُهُمۡ إِلَّا نُفُورٗا ﴾
[الإسرَاء: 41]

Ndithudi Ife tafotokoza chinthu chilichonse m’Korani iyi kuti iwo achenjezedwe, koma iyo siili kuonjezera chilichonse koma kuipidwa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولقد صرفنا في هذا القرآن ليذكروا وما يزيدهم إلا نفورا, باللغة نيانجا

﴿ولقد صرفنا في هذا القرآن ليذكروا وما يزيدهم إلا نفورا﴾ [الإسرَاء: 41]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo ndithu talongosola lamulo la chinthu chilichonse mwatsatanetsatane m’Qur’an iyi kuti akumbukire, ndipo (oipa) siikuwaonjezera (china) koma kuida ndi kuithawa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek