×

Nena, “Kukadakhala kuti kuli milungu ina yoonjezera pa Mulungu weniweni, monga momwe 17:42 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Isra’ ⮕ (17:42) ayat 42 in Chichewa

17:42 Surah Al-Isra’ ayat 42 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Isra’ ayat 42 - الإسرَاء - Page - Juz 15

﴿قُل لَّوۡ كَانَ مَعَهُۥٓ ءَالِهَةٞ كَمَا يَقُولُونَ إِذٗا لَّٱبۡتَغَوۡاْ إِلَىٰ ذِي ٱلۡعَرۡشِ سَبِيلٗا ﴾
[الإسرَاء: 42]

Nena, “Kukadakhala kuti kuli milungu ina yoonjezera pa Mulungu weniweni, monga momwe akunenera, iyo ikadapeza njira yoti ikhale pafupi ndi Mulungu.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قل لو كان معه آلهة كما يقولون إذا لابتغوا إلى ذي العرش, باللغة نيانجا

﴿قل لو كان معه آلهة كما يقولون إذا لابتغوا إلى ذي العرش﴾ [الإسرَاء: 42]

Khaled Ibrahim Betala
“Nena: “Pakadakhala milungu ina pamodzi ndi Allah, monga momwe akunenera, ikadafuna njira yomufikira (Mbuye) Mwini Arsh (Mpando wa chifumu, ndi kumthira nkhondo).”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek