×

Ndipo litadza pangano loyamba, Ife tidzakutumizirani akapolo athu a gulu la nkhondo 17:5 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Isra’ ⮕ (17:5) ayat 5 in Chichewa

17:5 Surah Al-Isra’ ayat 5 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Isra’ ayat 5 - الإسرَاء - Page - Juz 15

﴿فَإِذَا جَآءَ وَعۡدُ أُولَىٰهُمَا بَعَثۡنَا عَلَيۡكُمۡ عِبَادٗا لَّنَآ أُوْلِي بَأۡسٖ شَدِيدٖ فَجَاسُواْ خِلَٰلَ ٱلدِّيَارِۚ وَكَانَ وَعۡدٗا مَّفۡعُولٗا ﴾
[الإسرَاء: 5]

Ndipo litadza pangano loyamba, Ife tidzakutumizirani akapolo athu a gulu la nkhondo ankhongono zedi. Iwo amalowa m’katikati mwa nyumba zanu. Ndipo linali lonjezo limene linakwaniritsidwa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فإذا جاء وعد أولاهما بعثنا عليكم عبادا لنا أولي بأس شديد فجاسوا, باللغة نيانجا

﴿فإذا جاء وعد أولاهما بعثنا عليكم عبادا لنا أولي بأس شديد فجاسوا﴾ [الإسرَاء: 5]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo likadzafika lonjezo (lakupatsidwa chilango chakuononga) koyamba mkuononga kuwiriko, tidzawakhwirizira pa inu anthu athu, eni kumenya nkhondo mwaukali, adzakhala akuzungulira mkatikati mwa nyumba (zanu), ndipo lidali lonjezo lochitika
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek