×

Ife tidavumbulutsa kwa ana a Israyeli, m’Buku kuti, mosakayika, inu mudzabweretsa chisokonezo 17:4 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Isra’ ⮕ (17:4) ayat 4 in Chichewa

17:4 Surah Al-Isra’ ayat 4 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Isra’ ayat 4 - الإسرَاء - Page - Juz 15

﴿وَقَضَيۡنَآ إِلَىٰ بَنِيٓ إِسۡرَٰٓءِيلَ فِي ٱلۡكِتَٰبِ لَتُفۡسِدُنَّ فِي ٱلۡأَرۡضِ مَرَّتَيۡنِ وَلَتَعۡلُنَّ عُلُوّٗا كَبِيرٗا ﴾
[الإسرَاء: 4]

Ife tidavumbulutsa kwa ana a Israyeli, m’Buku kuti, mosakayika, inu mudzabweretsa chisokonezo padziko kachiwiri ndipo mudzakhala ankhanza ndi odzikweza kwambiri

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وقضينا إلى بني إسرائيل في الكتاب لتفسدن في الأرض مرتين ولتعلن علوا, باللغة نيانجا

﴿وقضينا إلى بني إسرائيل في الكتاب لتفسدن في الأرض مرتين ولتعلن علوا﴾ [الإسرَاء: 4]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo tidawazindikiritsa ana a Israyeli m’bukulo, kuti: “Ndithu inu muononga pa dziko kawiri, ndipo mudzapyola malire pochita zoipa, kupyola malire kwakukulu
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek