×

Ndithudi Korani ino imatsogolera ku zinthu zabwino ndipo imawauza anthu okhulupirira, amene 17:9 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Isra’ ⮕ (17:9) ayat 9 in Chichewa

17:9 Surah Al-Isra’ ayat 9 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Isra’ ayat 9 - الإسرَاء - Page - Juz 15

﴿إِنَّ هَٰذَا ٱلۡقُرۡءَانَ يَهۡدِي لِلَّتِي هِيَ أَقۡوَمُ وَيُبَشِّرُ ٱلۡمُؤۡمِنِينَ ٱلَّذِينَ يَعۡمَلُونَ ٱلصَّٰلِحَٰتِ أَنَّ لَهُمۡ أَجۡرٗا كَبِيرٗا ﴾
[الإسرَاء: 9]

Ndithudi Korani ino imatsogolera ku zinthu zabwino ndipo imawauza anthu okhulupirira, amene amachita zabwino, kuti adzakhala ndi malipiro aakulu

❮ Previous Next ❯

ترجمة: إن هذا القرآن يهدي للتي هي أقوم ويبشر المؤمنين الذين يعملون الصالحات, باللغة نيانجا

﴿إن هذا القرآن يهدي للتي هي أقوم ويبشر المؤمنين الذين يعملون الصالحات﴾ [الإسرَاء: 9]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndithu iyi Qur’an ikuongolera ku njira yoongoka ndi kuwasangalatsa okhulupirira omwe akuchita zabwino, kuti ndithu iwo adzalandira malipiro aakulu (pa tsiku la chiweruziro)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek