×

Mwina Ambuye wanu adzakuchitirani chifundo koma ngati inu mubwerera kuuchimo, nafenso tidzabwezera 17:8 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Isra’ ⮕ (17:8) ayat 8 in Chichewa

17:8 Surah Al-Isra’ ayat 8 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Isra’ ayat 8 - الإسرَاء - Page - Juz 15

﴿عَسَىٰ رَبُّكُمۡ أَن يَرۡحَمَكُمۡۚ وَإِنۡ عُدتُّمۡ عُدۡنَاۚ وَجَعَلۡنَا جَهَنَّمَ لِلۡكَٰفِرِينَ حَصِيرًا ﴾
[الإسرَاء: 8]

Mwina Ambuye wanu adzakuchitirani chifundo koma ngati inu mubwerera kuuchimo, nafenso tidzabwezera kukanthani. Ife takonza Gahena kukhala ndende ya anthu osakhulupirira

❮ Previous Next ❯

ترجمة: عسى ربكم أن يرحمكم وإن عدتم عدنا وجعلنا جهنم للكافرين حصيرا, باللغة نيانجا

﴿عسى ربكم أن يرحمكم وإن عدتم عدنا وجعلنا جهنم للكافرين حصيرا﴾ [الإسرَاء: 8]

Khaled Ibrahim Betala
““(Koma ngati mudzalungama mzochita zanu), Mbuye wanu adzakuchitirani chifundo; ndipo ngati mudzabwereranso (ku machitidwe anu okhota), tidzabwereranso (kukulangani). Ndipo taikonza Jahannam kukhala ndende ya osakhulupirira.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek