×

Amenewo ndiwo malipiro awo chifukwa iwo sadakhulupirire mawu athu ndipo adati, “Pamene 17:98 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Isra’ ⮕ (17:98) ayat 98 in Chichewa

17:98 Surah Al-Isra’ ayat 98 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Isra’ ayat 98 - الإسرَاء - Page - Juz 15

﴿ذَٰلِكَ جَزَآؤُهُم بِأَنَّهُمۡ كَفَرُواْ بِـَٔايَٰتِنَا وَقَالُوٓاْ أَءِذَا كُنَّا عِظَٰمٗا وَرُفَٰتًا أَءِنَّا لَمَبۡعُوثُونَ خَلۡقٗا جَدِيدًا ﴾
[الإسرَاء: 98]

Amenewo ndiwo malipiro awo chifukwa iwo sadakhulupirire mawu athu ndipo adati, “Pamene ife tidzasanduka mafupa ndi kufufutika, kodi tidzaukitsidwa kukhala chilengedwe chatsopano?”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ذلك جزاؤهم بأنهم كفروا بآياتنا وقالوا أئذا كنا عظاما ورفاتا أئنا لمبعوثون, باللغة نيانجا

﴿ذلك جزاؤهم بأنهم كفروا بآياتنا وقالوا أئذا كنا عظاما ورفاتا أئنا لمبعوثون﴾ [الإسرَاء: 98]

Khaled Ibrahim Betala
“(Chilango) chimenecho ndiyo mphoto yawo chifukwa cha kusakhulupirira kwawo zisonyezo (zomwe tidasonyeza kwa iwo), ndi kunena kwawo koti: “Kodi tikadzakhala mafupa ndi zidutswa zonyenyekanyenyeka, tidzaukitsidwanso kukhala zolengedwa zatsopano?”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek