×

Ndipo aliyense amene Mulungu wamutsogolera , atsogozedwa bwino koma iye amene Iye 17:97 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Isra’ ⮕ (17:97) ayat 97 in Chichewa

17:97 Surah Al-Isra’ ayat 97 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Isra’ ayat 97 - الإسرَاء - Page - Juz 15

﴿وَمَن يَهۡدِ ٱللَّهُ فَهُوَ ٱلۡمُهۡتَدِۖ وَمَن يُضۡلِلۡ فَلَن تَجِدَ لَهُمۡ أَوۡلِيَآءَ مِن دُونِهِۦۖ وَنَحۡشُرُهُمۡ يَوۡمَ ٱلۡقِيَٰمَةِ عَلَىٰ وُجُوهِهِمۡ عُمۡيٗا وَبُكۡمٗا وَصُمّٗاۖ مَّأۡوَىٰهُمۡ جَهَنَّمُۖ كُلَّمَا خَبَتۡ زِدۡنَٰهُمۡ سَعِيرٗا ﴾
[الإسرَاء: 97]

Ndipo aliyense amene Mulungu wamutsogolera , atsogozedwa bwino koma iye amene Iye amusocheza wotere iwe siungamupezere mtetezi wina aliyense kupatula Iye yekha. Ndipo Ife tidzawasonkhanitsa onse pa tsiku la kuuka kwa akufa, akuyenda pa nkhope zawo, akhungu, abububu ndi agonthi, malo awo adzakhala Gahena ndipo pamene malawi ake azikazima tizidzawaonjezera moto

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ومن يهد الله فهو المهتد ومن يضلل فلن تجد لهم أولياء من, باللغة نيانجا

﴿ومن يهد الله فهو المهتد ومن يضلل فلن تجد لهم أولياء من﴾ [الإسرَاء: 97]

❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek