×

Pamene anyamata adathawa ndipo adalowa ndi cholinga chopeza malo kuphanga ndipo adati, 18:10 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Kahf ⮕ (18:10) ayat 10 in Chichewa

18:10 Surah Al-Kahf ayat 10 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Kahf ayat 10 - الكَهف - Page - Juz 15

﴿إِذۡ أَوَى ٱلۡفِتۡيَةُ إِلَى ٱلۡكَهۡفِ فَقَالُواْ رَبَّنَآ ءَاتِنَا مِن لَّدُنكَ رَحۡمَةٗ وَهَيِّئۡ لَنَا مِنۡ أَمۡرِنَا رَشَدٗا ﴾
[الكَهف: 10]

Pamene anyamata adathawa ndipo adalowa ndi cholinga chopeza malo kuphanga ndipo adati, “Ambuye wathu! Tionetseni chisoni chochokera kwa Inu ndipo tikonzereni zinthu zathu munjira zoyenera.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: إذ أوى الفتية إلى الكهف فقالوا ربنا آتنا من لدنك رحمة وهيئ, باللغة نيانجا

﴿إذ أوى الفتية إلى الكهف فقالوا ربنا آتنا من لدنك رحمة وهيئ﴾ [الكَهف: 10]

Khaled Ibrahim Betala
“Pamene anyamata adathawira kuphanga nati: “Mbuye wathu! Tipatseni chifundo chochokera kwa Inu, ndipo tikonzereni chiongoko m’zochita zathu.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek