×

Ife tili kukuuza nkhani zawo zonse mwachoonadi. Ndithudi! Iwo anali anyamata amene 18:13 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Kahf ⮕ (18:13) ayat 13 in Chichewa

18:13 Surah Al-Kahf ayat 13 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Kahf ayat 13 - الكَهف - Page - Juz 15

﴿نَّحۡنُ نَقُصُّ عَلَيۡكَ نَبَأَهُم بِٱلۡحَقِّۚ إِنَّهُمۡ فِتۡيَةٌ ءَامَنُواْ بِرَبِّهِمۡ وَزِدۡنَٰهُمۡ هُدٗى ﴾
[الكَهف: 13]

Ife tili kukuuza nkhani zawo zonse mwachoonadi. Ndithudi! Iwo anali anyamata amene adakhulupirira mwa Ambuye wawo, ndipo Ife tidawaonjezera malangizo

❮ Previous Next ❯

ترجمة: نحن نقص عليك نبأهم بالحق إنهم فتية آمنوا بربهم وزدناهم هدى, باللغة نيانجا

﴿نحن نقص عليك نبأهم بالحق إنهم فتية آمنوا بربهم وزدناهم هدى﴾ [الكَهف: 13]

Khaled Ibrahim Betala
“Ife tikusimbira (iwe mtumiki{s.a.w}) nkhani zawo mwachoonadi; ndithu iwo adali anyamata amene adakhulupirira Mbuye wawo, ndipo tidawaonjezera chiongoko
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek