×

Ndipo Iye adali ndi zipatso zambiri ndipo adanena kwa mnzake pamene anali 18:34 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Kahf ⮕ (18:34) ayat 34 in Chichewa

18:34 Surah Al-Kahf ayat 34 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Kahf ayat 34 - الكَهف - Page - Juz 15

﴿وَكَانَ لَهُۥ ثَمَرٞ فَقَالَ لِصَٰحِبِهِۦ وَهُوَ يُحَاوِرُهُۥٓ أَنَا۠ أَكۡثَرُ مِنكَ مَالٗا وَأَعَزُّ نَفَرٗا ﴾
[الكَهف: 34]

Ndipo Iye adali ndi zipatso zambiri ndipo adanena kwa mnzake pamene anali kutsutsana naye nati, “Ine ndili ndi chuma chambiri kuposa iwe ndiponso ndili ndi anthu a ntchito amphamvu kwambiri.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وكان له ثمر فقال لصاحبه وهو يحاوره أنا أكثر منك مالا وأعز, باللغة نيانجا

﴿وكان له ثمر فقال لصاحبه وهو يحاوره أنا أكثر منك مالا وأعز﴾ [الكَهف: 34]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo iye adali ndi chuma (china) nati kwa mnzakeyo mokambirana naye: “Ine ndili ndi chuma chambiri kuposa iwe, (ndilinso) ndi mphamvu zambiri chifukwa cha onditsatira (omwe ndili nawo).”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek