×

Chuma ndi ana ndi zinthu zokongola za umoyo wadziko lapansi. Koma ntchito 18:46 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Kahf ⮕ (18:46) ayat 46 in Chichewa

18:46 Surah Al-Kahf ayat 46 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Kahf ayat 46 - الكَهف - Page - Juz 15

﴿ٱلۡمَالُ وَٱلۡبَنُونَ زِينَةُ ٱلۡحَيَوٰةِ ٱلدُّنۡيَاۖ وَٱلۡبَٰقِيَٰتُ ٱلصَّٰلِحَٰتُ خَيۡرٌ عِندَ رَبِّكَ ثَوَابٗا وَخَيۡرٌ أَمَلٗا ﴾
[الكَهف: 46]

Chuma ndi ana ndi zinthu zokongola za umoyo wadziko lapansi. Koma ntchito zabwino zokhalitsa ndi zomwe zili ndi malipiro abwino kwa Ambuye wako ndi chiyembekezo chabwino

❮ Previous Next ❯

ترجمة: المال والبنون زينة الحياة الدنيا والباقيات الصالحات خير عند ربك ثوابا وخير, باللغة نيانجا

﴿المال والبنون زينة الحياة الدنيا والباقيات الصالحات خير عند ربك ثوابا وخير﴾ [الكَهف: 46]

Khaled Ibrahim Betala
“Chuma ndi ana ndizokometsera za moyo wa dziko lapansi, koma ntchito zabwino zopitirira ndizo zabwino kwa Mbuye wako, monga mphoto ndi chiyembekezo chabwino
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek