×

Ndipo Ife sitimangotumiza Atumwi kupatula kuti akalalikire nkhani yabwino ndi kupereka chenjezo. 18:56 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Kahf ⮕ (18:56) ayat 56 in Chichewa

18:56 Surah Al-Kahf ayat 56 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Kahf ayat 56 - الكَهف - Page - Juz 15

﴿وَمَا نُرۡسِلُ ٱلۡمُرۡسَلِينَ إِلَّا مُبَشِّرِينَ وَمُنذِرِينَۚ وَيُجَٰدِلُ ٱلَّذِينَ كَفَرُواْ بِٱلۡبَٰطِلِ لِيُدۡحِضُواْ بِهِ ٱلۡحَقَّۖ وَٱتَّخَذُوٓاْ ءَايَٰتِي وَمَآ أُنذِرُواْ هُزُوٗا ﴾
[الكَهف: 56]

Ndipo Ife sitimangotumiza Atumwi kupatula kuti akalalikire nkhani yabwino ndi kupereka chenjezo. Koma anthu osakhulupirira amatsutsa mwabodza kuti agonjetse choonadi ndi bodza lawo. Ndipo iwo amasandutsa mawu anga ndi zonse zomwe achenjezedwa ngati nthabwala kapenachoseketsa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وما نرسل المرسلين إلا مبشرين ومنذرين ويجادل الذين كفروا بالباطل ليدحضوا به, باللغة نيانجا

﴿وما نرسل المرسلين إلا مبشرين ومنذرين ويجادل الذين كفروا بالباطل ليدحضوا به﴾ [الكَهف: 56]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndiponso sitituma atumiki (ndi cholinga choti adzetse chilango), koma kuti akhale onena nkhani zabwino ndi ochenjeza. Ndipo amene sadakhulupirire, akuchita makani ndi chabodza kuti kupyolera m’chabodzacho achotse choonadi, ndipo Ayah Zanga ndi zomwe achenjezedwa nazo, akuzichitira chipongwe
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek