×

Motero iwo adanyamuka ndipo pamene iwo adakwera m’chombo, mnzake wa Mose adaboola 18:71 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Kahf ⮕ (18:71) ayat 71 in Chichewa

18:71 Surah Al-Kahf ayat 71 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Kahf ayat 71 - الكَهف - Page - Juz 15

﴿فَٱنطَلَقَا حَتَّىٰٓ إِذَا رَكِبَا فِي ٱلسَّفِينَةِ خَرَقَهَاۖ قَالَ أَخَرَقۡتَهَا لِتُغۡرِقَ أَهۡلَهَا لَقَدۡ جِئۡتَ شَيۡـًٔا إِمۡرٗا ﴾
[الكَهف: 71]

Motero iwo adanyamuka ndipo pamene iwo adakwera m’chombo, mnzake wa Mose adaboola chombocho. Mose adati, “Kodi waboola dzenje pa chombochi ndi cholinga chofuna kumiza eni ake? Ndithudi ichi ndi chinthu choipa kwambiri chimene wachita!”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فانطلقا حتى إذا ركبا في السفينة خرقها قال أخرقتها لتغرق أهلها لقد, باللغة نيانجا

﴿فانطلقا حتى إذا ركبا في السفينة خرقها قال أخرقتها لتغرق أهلها لقد﴾ [الكَهف: 71]

Khaled Ibrahim Betala
“Choncho onse awiri adanyamuka kufikira pamene adakakwera m’chombo adachiboola. (Mûsa) adati: “Kodi wachiboola kuti uwamize ali m’menemo? Ndithu wachita chinthu chachikulu choipa.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek