×

Mose adati, “Ngati ine ndikufunsanso chinthu china pambuyo pa izi, usayende nanenso 18:76 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Kahf ⮕ (18:76) ayat 76 in Chichewa

18:76 Surah Al-Kahf ayat 76 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Kahf ayat 76 - الكَهف - Page - Juz 16

﴿قَالَ إِن سَأَلۡتُكَ عَن شَيۡءِۭ بَعۡدَهَا فَلَا تُصَٰحِبۡنِيۖ قَدۡ بَلَغۡتَ مِن لَّدُنِّي عُذۡرٗا ﴾
[الكَهف: 76]

Mose adati, “Ngati ine ndikufunsanso chinthu china pambuyo pa izi, usayende nanenso chifukwa ukhala utachipeza chifukwa kuchokera mwa ine.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قال إن سألتك عن شيء بعدها فلا تصاحبني قد بلغت من لدني, باللغة نيانجا

﴿قال إن سألتك عن شيء بعدها فلا تصاحبني قد بلغت من لدني﴾ [الكَهف: 76]

Khaled Ibrahim Betala
“(Mûsa) adati: “Ngati ndikufunsanso chilichonse pambuyo pa ichi, usandilole kutsagana nawe. Ndiye kuti wakwaniritsa dandaulo lako pa ine.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek