×

Ndipo tidafuna kuti Ambuye wawo awapatse m’malo mwake, mwana wina wabwino ndi 18:81 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Kahf ⮕ (18:81) ayat 81 in Chichewa

18:81 Surah Al-Kahf ayat 81 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Kahf ayat 81 - الكَهف - Page - Juz 16

﴿فَأَرَدۡنَآ أَن يُبۡدِلَهُمَا رَبُّهُمَا خَيۡرٗا مِّنۡهُ زَكَوٰةٗ وَأَقۡرَبَ رُحۡمٗا ﴾
[الكَهف: 81]

Ndipo tidafuna kuti Ambuye wawo awapatse m’malo mwake, mwana wina wabwino ndi woyera mtima kuposa iye

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فأردنا أن يبدلهما ربهما خيرا منه زكاة وأقرب رحما, باللغة نيانجا

﴿فأردنا أن يبدلهما ربهما خيرا منه زكاة وأقرب رحما﴾ [الكَهف: 81]

Khaled Ibrahim Betala
“Choncho tidafuna kuti Mbuye wawo awasinthire ndi wabwino kuposa iye pa kuyera, ndi wachifundo chapafupi (kwa makolo ake.)”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek