×

Mpaka pamene adafika polowera dzuwa ndipo adalipeza dzuwalo lili kulowa m’dziwe la 18:86 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Kahf ⮕ (18:86) ayat 86 in Chichewa

18:86 Surah Al-Kahf ayat 86 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Kahf ayat 86 - الكَهف - Page - Juz 16

﴿حَتَّىٰٓ إِذَا بَلَغَ مَغۡرِبَ ٱلشَّمۡسِ وَجَدَهَا تَغۡرُبُ فِي عَيۡنٍ حَمِئَةٖ وَوَجَدَ عِندَهَا قَوۡمٗاۖ قُلۡنَا يَٰذَا ٱلۡقَرۡنَيۡنِ إِمَّآ أَن تُعَذِّبَ وَإِمَّآ أَن تَتَّخِذَ فِيهِمۡ حُسۡنٗا ﴾
[الكَهف: 86]

Mpaka pamene adafika polowera dzuwa ndipo adalipeza dzuwalo lili kulowa m’dziwe la matope akuda. Pafupi pomwepo iye adapeza anthu ena. Ife tidati, “Iwe Dhul-Qarnain! Iwe uli ndi ufulu wowalanga kapena wowachitira chisoni.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: حتى إذا بلغ مغرب الشمس وجدها تغرب في عين حمئة ووجد عندها, باللغة نيانجا

﴿حتى إذا بلغ مغرب الشمس وجدها تغرب في عين حمئة ووجد عندها﴾ [الكَهف: 86]

Khaled Ibrahim Betala
“Mpaka pomwe adafika kumlowero kwa dzuwa (ku maiko a kuzambwe), adaliona (ngati) likulowa pa dziwe la matope ambiri. Ndipo pompo adapeza anthu; tidati: “E iwe Thul-Qarnain! Alange, kapena achitire zabwino.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek