×

Iye adati, “Akakhala iye amene achita zoipa, tidzamulanga ndipo iye adzabwezedwa kwa 18:87 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Kahf ⮕ (18:87) ayat 87 in Chichewa

18:87 Surah Al-Kahf ayat 87 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Kahf ayat 87 - الكَهف - Page - Juz 16

﴿قَالَ أَمَّا مَن ظَلَمَ فَسَوۡفَ نُعَذِّبُهُۥ ثُمَّ يُرَدُّ إِلَىٰ رَبِّهِۦ فَيُعَذِّبُهُۥ عَذَابٗا نُّكۡرٗا ﴾
[الكَهف: 87]

Iye adati, “Akakhala iye amene achita zoipa, tidzamulanga ndipo iye adzabwezedwa kwa Ambuye wake yemwe adzamulanga ndi chilango choipa kwambiri.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قال أما من ظلم فسوف نعذبه ثم يرد إلى ربه فيعذبه عذابا, باللغة نيانجا

﴿قال أما من ظلم فسوف نعذبه ثم يرد إلى ربه فيعذبه عذابا﴾ [الكَهف: 87]

Khaled Ibrahim Betala
“Adati: “Koma amene achita zosalungama timulanga; ndipo kenako adzabwezedwa kwa Mbuye wake; ndipo akamukhaulitsa ndi chilango choipa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek