×

Ndipatseni zidutswa zachitsulo; mpaka pamene iye adadzadza gawo limene linali pakati pa 18:96 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Kahf ⮕ (18:96) ayat 96 in Chichewa

18:96 Surah Al-Kahf ayat 96 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Kahf ayat 96 - الكَهف - Page - Juz 16

﴿ءَاتُونِي زُبَرَ ٱلۡحَدِيدِۖ حَتَّىٰٓ إِذَا سَاوَىٰ بَيۡنَ ٱلصَّدَفَيۡنِ قَالَ ٱنفُخُواْۖ حَتَّىٰٓ إِذَا جَعَلَهُۥ نَارٗا قَالَ ءَاتُونِيٓ أُفۡرِغۡ عَلَيۡهِ قِطۡرٗا ﴾
[الكَهف: 96]

Ndipatseni zidutswa zachitsulo; mpaka pamene iye adadzadza gawo limene linali pakati pa mapiriwa. Iye adati, “Uzirani ndi livumbo lanu.” Pamene adazifiwiritsa zidutswazo ngati moto, iye adati, “Ndipatseni mtovu kuti ndiuthire pa zidutswazo.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: آتوني زبر الحديد حتى إذا ساوى بين الصدفين قال انفخوا حتى إذا, باللغة نيانجا

﴿آتوني زبر الحديد حتى إذا ساوى بين الصدفين قال انفخوا حتى إذا﴾ [الكَهف: 96]

Khaled Ibrahim Betala
““Ndipatseni zidutswa za zitsulo.” Kufikira pamene adadzaza ndi zitsulozo mpata umene udalipo pakati pa mapiri awiriwo, adati: “Pemelerani (moto).” Mpaka (chitsulocho) chidafiira monga moto, adati: “Ndibweretsereni mtovu wosungunuka ndiuthire pamwamba pake (pa chitsulocho).”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek