Quran with Chichewa translation - Surah Maryam ayat 10 - مَريَم - Page - Juz 16
﴿قَالَ رَبِّ ٱجۡعَل لِّيٓ ءَايَةٗۖ قَالَ ءَايَتُكَ أَلَّا تُكَلِّمَ ٱلنَّاسَ ثَلَٰثَ لَيَالٖ سَوِيّٗا ﴾
[مَريَم: 10]
﴿قال رب اجعل لي آية قال آيتك ألا تكلم الناس ثلاث ليال﴾ [مَريَم: 10]
Khaled Ibrahim Betala “Adati: “Mbuye wanga ndipatseni chizindikiro (chodziwitsa kuti mkazi wanga ali ndi pakati).” Adati: “Chizindikiro chako ndikuti sudzatha kuyankhula ndi anthu mpaka masiku atatu pomwe iwe uli bwinobwino.” |