Quran with Chichewa translation - Surah Maryam ayat 43 - مَريَم - Page - Juz 16
﴿يَٰٓأَبَتِ إِنِّي قَدۡ جَآءَنِي مِنَ ٱلۡعِلۡمِ مَا لَمۡ يَأۡتِكَ فَٱتَّبِعۡنِيٓ أَهۡدِكَ صِرَٰطٗا سَوِيّٗا ﴾
[مَريَم: 43]
﴿ياأبت إني قد جاءني من العلم ما لم يأتك فاتبعني أهدك صراطا﴾ [مَريَم: 43]
Khaled Ibrahim Betala ““E inu bambo wanga! Ndithu ine zandidzera nzeru (zomuzindikira Allah) zomwe sizidakudzereni; choncho nditsateni. Ndikutsogolereni ku njira yolungama.” |