×

Ndipo pamene Abrahamu adasiya anthu ake ndi mafano amene iwo anali kupembedza 19:49 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Maryam ⮕ (19:49) ayat 49 in Chichewa

19:49 Surah Maryam ayat 49 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Maryam ayat 49 - مَريَم - Page - Juz 16

﴿فَلَمَّا ٱعۡتَزَلَهُمۡ وَمَا يَعۡبُدُونَ مِن دُونِ ٱللَّهِ وَهَبۡنَا لَهُۥٓ إِسۡحَٰقَ وَيَعۡقُوبَۖ وَكُلّٗا جَعَلۡنَا نَبِيّٗا ﴾
[مَريَم: 49]

Ndipo pamene Abrahamu adasiya anthu ake ndi mafano amene iwo anali kupembedza kuonjezera pa Mulungu, tidamupatsa Isake ndi Yakobo. Aliyense wa iwo tidamupanga kukhala Mtumwi

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فلما اعتزلهم وما يعبدون من دون الله وهبنا له إسحاق ويعقوب وكلا, باللغة نيانجا

﴿فلما اعتزلهم وما يعبدون من دون الله وهبنا له إسحاق ويعقوب وكلا﴾ [مَريَم: 49]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo pamene adawapatukira ndi zimene adali kuzipembedza kusiya Allah, tidampatsa iye Ishaq, ndi Ya’qub, ndipo aliyense wa iwo tidampanga kukhala m’neneri
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek