Quran with Chichewa translation - Surah Maryam ayat 50 - مَريَم - Page - Juz 16
﴿وَوَهَبۡنَا لَهُم مِّن رَّحۡمَتِنَا وَجَعَلۡنَا لَهُمۡ لِسَانَ صِدۡقٍ عَلِيّٗا ﴾
[مَريَم: 50]
﴿ووهبنا لهم من رحمتنا وجعلنا لهم لسان صدق عليا﴾ [مَريَم: 50]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo tidawapatsa iwo chifundo Chathu, ndi kuwayikira iwo kutchulidwa kwabwino, kwapamwamba (pakati pa zolengedwa) |