×

Motero Ife tapanga iyo kukhala yosavuta ya m’chiyankhulo chako kuti upeleke nkhani 19:97 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Maryam ⮕ (19:97) ayat 97 in Chichewa

19:97 Surah Maryam ayat 97 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Maryam ayat 97 - مَريَم - Page - Juz 16

﴿فَإِنَّمَا يَسَّرۡنَٰهُ بِلِسَانِكَ لِتُبَشِّرَ بِهِ ٱلۡمُتَّقِينَ وَتُنذِرَ بِهِۦ قَوۡمٗا لُّدّٗا ﴾
[مَريَم: 97]

Motero Ife tapanga iyo kukhala yosavuta ya m’chiyankhulo chako kuti upeleke nkhani yabwino kwa anthu oopa ndi kuchenjeza ndi ilo anthu otsutsa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فإنما يسرناه بلسانك لتبشر به المتقين وتنذر به قوما لدا, باللغة نيانجا

﴿فإنما يسرناه بلسانك لتبشر به المتقين وتنذر به قوما لدا﴾ [مَريَم: 97]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndithu taifewetsa (Qur’an) m’chiyankhulo chako kuti ndi iyo uwawuze nkhani zabwino oopa Allah ndipo ndi iyo uwachenjeze anthu amakani
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek