×

Ndipo iwo amene adali kuwatsatira adzati: “Kukanakhala kuti tikadatha kubwereranso, Ife tikadawakana 2:167 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:167) ayat 167 in Chichewa

2:167 Surah Al-Baqarah ayat 167 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 167 - البَقَرَة - Page - Juz 2

﴿وَقَالَ ٱلَّذِينَ ٱتَّبَعُواْ لَوۡ أَنَّ لَنَا كَرَّةٗ فَنَتَبَرَّأَ مِنۡهُمۡ كَمَا تَبَرَّءُواْ مِنَّاۗ كَذَٰلِكَ يُرِيهِمُ ٱللَّهُ أَعۡمَٰلَهُمۡ حَسَرَٰتٍ عَلَيۡهِمۡۖ وَمَا هُم بِخَٰرِجِينَ مِنَ ٱلنَّارِ ﴾
[البَقَرَة: 167]

Ndipo iwo amene adali kuwatsatira adzati: “Kukanakhala kuti tikadatha kubwereranso, Ife tikadawakana monga momwe atikanira ife tsopano.” Motero Mulungu adzawaonetsa ntchito zawo kukhala zinthu zopanda pake. Ndipo sipadzakhala njira yothawira ku moto

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وقال الذين اتبعوا لو أن لنا كرة فنتبرأ منهم كما تبرءوا منا, باللغة نيانجا

﴿وقال الذين اتبعوا لو أن لنا كرة فنتبرأ منهم كما تبرءوا منا﴾ [البَقَرَة: 167]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo otsatirawo adzati: “Kukadakhala kotheka kwa ife kubwerera (ku moyo wa pa dziko) tikadawakana monga iwo atikanira.” Umo ndi momwe Allah adzikawaonetsera zochita zawo kukhala madandaulo awo. Ndipo iwo sadzatulukanso ku Moto
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek