×

Mwezi Woyera ndi Mwezi Woyera ndipo zinthu zosaloledwa nazonso zimabwezeredwa. Ndipo aliyense 2:194 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:194) ayat 194 in Chichewa

2:194 Surah Al-Baqarah ayat 194 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 194 - البَقَرَة - Page - Juz 2

﴿ٱلشَّهۡرُ ٱلۡحَرَامُ بِٱلشَّهۡرِ ٱلۡحَرَامِ وَٱلۡحُرُمَٰتُ قِصَاصٞۚ فَمَنِ ٱعۡتَدَىٰ عَلَيۡكُمۡ فَٱعۡتَدُواْ عَلَيۡهِ بِمِثۡلِ مَا ٱعۡتَدَىٰ عَلَيۡكُمۡۚ وَٱتَّقُواْ ٱللَّهَ وَٱعۡلَمُوٓاْ أَنَّ ٱللَّهَ مَعَ ٱلۡمُتَّقِينَ ﴾
[البَقَرَة: 194]

Mwezi Woyera ndi Mwezi Woyera ndipo zinthu zosaloledwa nazonso zimabwezeredwa. Ndipo aliyense amene akuputani mubwezereni molingana ndi mmene wachitira iye. Ndipo muopeni Mulungu ndipo dziwani kuti Mulungu ali pamodzi ndi iwo amene amalewa zoipa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: الشهر الحرام بالشهر الحرام والحرمات قصاص فمن اعتدى عليكم فاعتدوا عليه بمثل, باللغة نيانجا

﴿الشهر الحرام بالشهر الحرام والحرمات قصاص فمن اعتدى عليكم فاعتدوا عليه بمثل﴾ [البَقَرَة: 194]

Khaled Ibrahim Betala
“Mwezi wopatulika kwa mwezi wopatulika; ndipo zinthu zopatulika paikidwa kubwezerana. Ndipo amene wakuchitirani mtopola, inunso mchitireni mtopola molingana ndi momwe wakuchitirani mtopola, ndipo opani Allah (musapyoze kuposa momwe wakuchitirani). Ndipo dziwani kuti Allah ali pamodzi ndi oopa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek