×

Ngati munthu asudzula mkazi wake kachitatu, iye saloledwa kumukwatiranso pokhapokha ngati atakwatiwa 2:230 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:230) ayat 230 in Chichewa

2:230 Surah Al-Baqarah ayat 230 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 230 - البَقَرَة - Page - Juz 2

﴿فَإِن طَلَّقَهَا فَلَا تَحِلُّ لَهُۥ مِنۢ بَعۡدُ حَتَّىٰ تَنكِحَ زَوۡجًا غَيۡرَهُۥۗ فَإِن طَلَّقَهَا فَلَا جُنَاحَ عَلَيۡهِمَآ أَن يَتَرَاجَعَآ إِن ظَنَّآ أَن يُقِيمَا حُدُودَ ٱللَّهِۗ وَتِلۡكَ حُدُودُ ٱللَّهِ يُبَيِّنُهَا لِقَوۡمٖ يَعۡلَمُونَ ﴾
[البَقَرَة: 230]

Ngati munthu asudzula mkazi wake kachitatu, iye saloledwa kumukwatiranso pokhapokha ngati atakwatiwa ndi mwamuna wina ndipo mwamunayo amusudzulanso. Sicholakwa kwa iwo kubwererana, ngati iwo atsimikiza kuti adzasunga malamulo a Mulungu. Amenewa ndi malamulo a Mulungu amene akuwaonetsa poyera kwa anthu ozindikira

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فإن طلقها فلا تحل له من بعد حتى تنكح زوجا غيره فإن, باللغة نيانجا

﴿فإن طلقها فلا تحل له من بعد حتى تنكح زوجا غيره فإن﴾ [البَقَرَة: 230]

❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek