×

Kodi iwe siudawone zimene gulu la ana a Israyeli adachita Mose atafa? 2:246 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:246) ayat 246 in Chichewa

2:246 Surah Al-Baqarah ayat 246 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 246 - البَقَرَة - Page - Juz 2

﴿أَلَمۡ تَرَ إِلَى ٱلۡمَلَإِ مِنۢ بَنِيٓ إِسۡرَٰٓءِيلَ مِنۢ بَعۡدِ مُوسَىٰٓ إِذۡ قَالُواْ لِنَبِيّٖ لَّهُمُ ٱبۡعَثۡ لَنَا مَلِكٗا نُّقَٰتِلۡ فِي سَبِيلِ ٱللَّهِۖ قَالَ هَلۡ عَسَيۡتُمۡ إِن كُتِبَ عَلَيۡكُمُ ٱلۡقِتَالُ أَلَّا تُقَٰتِلُواْۖ قَالُواْ وَمَا لَنَآ أَلَّا نُقَٰتِلَ فِي سَبِيلِ ٱللَّهِ وَقَدۡ أُخۡرِجۡنَا مِن دِيَٰرِنَا وَأَبۡنَآئِنَاۖ فَلَمَّا كُتِبَ عَلَيۡهِمُ ٱلۡقِتَالُ تَوَلَّوۡاْ إِلَّا قَلِيلٗا مِّنۡهُمۡۚ وَٱللَّهُ عَلِيمُۢ بِٱلظَّٰلِمِينَ ﴾
[البَقَرَة: 246]

Kodi iwe siudawone zimene gulu la ana a Israyeli adachita Mose atafa? Pamene iwo adati kwa Mtumwi wawo: “Tisankhire Mfumu,” ndipo ife tidzamenya nkhondo m’njira ya Mulungu. Iye adati: “Kodi inu simungamenye nkhondo ngati mutalamulidwa kutero?” Iwo adati: “Kodi ife tingakane bwanji kumenya nkhondo mmene afunira Mulungu pamene ife tidaumilizidwa kuchoka m’nyumba mwathu ndi kusiya ana athu?” Koma pamene adalamulidwa kuti amenye nkhondo, onse adathawa kupatula anthu owerengeka okha. Ndipo Mulungu amadziwa anthu osalungama

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ألم تر إلى الملإ من بني إسرائيل من بعد موسى إذ قالوا, باللغة نيانجا

﴿ألم تر إلى الملإ من بني إسرائيل من بعد موسى إذ قالوا﴾ [البَقَرَة: 246]

Khaled Ibrahim Betala
“Kodi sudamve nkhani ya akuluakulu a ana a Israyeli pambuyo pa Mûsa? Adanena kwa mneneri wawo: “Tidzozere mfumu kuti timenye nkhondo pa njira ya Allah.” Iye (mneneri wawoyo) adati: “Mwinatu simungamenye nkhondoyo ngati kutalamulidwa kwa inu. (Iwo) adati: “Nchotani kuti tisamenye nkhondo pa njira ya Allah pomwe tatulutsidwa m’nyumba zathu pamodzi ndi ana athu?” Koma pamene adalamulidwa kumenya nkhondoyo, adatembenuka, kupatula ochepa mwa iwo. Ndipo Allah akudziwa bwinobwino za anthu ochita zoipa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek