×

Iye amapereka luntha kwa iye amene wamufuna ndipo iye amene wapatsidwa luntha, 2:269 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:269) ayat 269 in Chichewa

2:269 Surah Al-Baqarah ayat 269 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 269 - البَقَرَة - Page - Juz 3

﴿يُؤۡتِي ٱلۡحِكۡمَةَ مَن يَشَآءُۚ وَمَن يُؤۡتَ ٱلۡحِكۡمَةَ فَقَدۡ أُوتِيَ خَيۡرٗا كَثِيرٗاۗ وَمَا يَذَّكَّرُ إِلَّآ أُوْلُواْ ٱلۡأَلۡبَٰبِ ﴾
[البَقَرَة: 269]

Iye amapereka luntha kwa iye amene wamufuna ndipo iye amene wapatsidwa luntha, ndithudi, wapatsidwa chinthu chabwino kwambiri. Koma palibe wina aliyense amene amakumbukira kupatula anthu ozindikira

❮ Previous Next ❯

ترجمة: يؤتي الحكمة من يشاء ومن يؤت الحكمة فقد أوتي خيرا كثيرا وما, باللغة نيانجا

﴿يؤتي الحكمة من يشاء ومن يؤت الحكمة فقد أوتي خيرا كثيرا وما﴾ [البَقَرَة: 269]

Khaled Ibrahim Betala
“Amapatsa nzeru (zothandiza) amene wamfuna; ndipo amene wapatsidwa nzeru, ndithudi, wapatsidwa zabwino zambiri. Ndipo (zoterezi) sakumbukira koma eni nzeru okha
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek