Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 270 - البَقَرَة - Page - Juz 3
﴿وَمَآ أَنفَقۡتُم مِّن نَّفَقَةٍ أَوۡ نَذَرۡتُم مِّن نَّذۡرٖ فَإِنَّ ٱللَّهَ يَعۡلَمُهُۥۗ وَمَا لِلظَّٰلِمِينَ مِنۡ أَنصَارٍ ﴾ 
[البَقَرَة: 270]
﴿وما أنفقتم من نفقة أو نذرتم من نذر فإن الله يعلمه وما﴾ [البَقَرَة: 270]
| Khaled Ibrahim Betala “Ndipo chilichonse chomwe mungapereke kapena naziri (lonjezo) iliyonse yomwe mwalonjeza Allah, ndithudi, Allah akudziwa zonsezi. Ndipo anthu ochita zoipa sadzakhala ndi athandizi |