×

Ndithudi onse amene ali ndi chikhulupiriro ndipo amachita ntchito zabwino, amasamala mapemphero 2:277 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:277) ayat 277 in Chichewa

2:277 Surah Al-Baqarah ayat 277 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 277 - البَقَرَة - Page - Juz 3

﴿إِنَّ ٱلَّذِينَ ءَامَنُواْ وَعَمِلُواْ ٱلصَّٰلِحَٰتِ وَأَقَامُواْ ٱلصَّلَوٰةَ وَءَاتَوُاْ ٱلزَّكَوٰةَ لَهُمۡ أَجۡرُهُمۡ عِندَ رَبِّهِمۡ وَلَا خَوۡفٌ عَلَيۡهِمۡ وَلَا هُمۡ يَحۡزَنُونَ ﴾
[البَقَرَة: 277]

Ndithudi onse amene ali ndi chikhulupiriro ndipo amachita ntchito zabwino, amasamala mapemphero awo ndi kupereka chopereka chothandizira anthu osauka, adzalipidwa ndi Ambuye wawo. Ndipo iwo sadzaopa china chilichonse kapena kudandaula

❮ Previous Next ❯

ترجمة: إن الذين آمنوا وعملوا الصالحات وأقاموا الصلاة وآتوا الزكاة لهم أجرهم عند, باللغة نيانجا

﴿إن الذين آمنوا وعملوا الصالحات وأقاموا الصلاة وآتوا الزكاة لهم أجرهم عند﴾ [البَقَرَة: 277]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndithudi, amene akhulupirira, nachita zabwino, napemphera Swala moyenera ndi kupereka chopereka (Zakaat), iwo akapeza malipiro awo kwa Mbuye wawo. Ndipo pa iwo sipadzakhala mantha ndiponso sadzadandaula
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek