×

Amene amakhulupirira mu chinthu chosaoneka ndipo amapemphera pa nthawi yake ndipo amapereka 2:3 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:3) ayat 3 in Chichewa

2:3 Surah Al-Baqarah ayat 3 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 3 - البَقَرَة - Page - Juz 1

﴿ٱلَّذِينَ يُؤۡمِنُونَ بِٱلۡغَيۡبِ وَيُقِيمُونَ ٱلصَّلَوٰةَ وَمِمَّا رَزَقۡنَٰهُمۡ يُنفِقُونَ ﴾
[البَقَرَة: 3]

Amene amakhulupirira mu chinthu chosaoneka ndipo amapemphera pa nthawi yake ndipo amapereka kwa anthu osowa zina mwa zinthu zimene tawapatsa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: الذين يؤمنون بالغيب ويقيمون الصلاة ومما رزقناهم ينفقون, باللغة نيانجا

﴿الذين يؤمنون بالغيب ويقيمون الصلاة ومما رزقناهم ينفقون﴾ [البَقَرَة: 3]

Khaled Ibrahim Betala
“Omwe amakhulupirira zosaoneka ndi maso (monga Munda wamtendere, Moto, Angelo ndi zina zotere zomwe Allah ndi Mtumiki (s.a.w) adazifotokoza, amapemphera Swala moyenera, ndiponso amapereka m’zimene tawapatsa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek