×

Ndipo Mulungu adati: “Iwe Adamu! Auze mayina ake.” Ndipo pamene iye adatchula 2:33 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:33) ayat 33 in Chichewa

2:33 Surah Al-Baqarah ayat 33 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 33 - البَقَرَة - Page - Juz 1

﴿قَالَ يَٰٓـَٔادَمُ أَنۢبِئۡهُم بِأَسۡمَآئِهِمۡۖ فَلَمَّآ أَنۢبَأَهُم بِأَسۡمَآئِهِمۡ قَالَ أَلَمۡ أَقُل لَّكُمۡ إِنِّيٓ أَعۡلَمُ غَيۡبَ ٱلسَّمَٰوَٰتِ وَٱلۡأَرۡضِ وَأَعۡلَمُ مَا تُبۡدُونَ وَمَا كُنتُمۡ تَكۡتُمُونَ ﴾
[البَقَرَة: 33]

Ndipo Mulungu adati: “Iwe Adamu! Auze mayina ake.” Ndipo pamene iye adatchula mayina a zinthuzo, Mulungu adati: “Kodi Ine sindidakuuzeni inu kuti Ine ndimadziwa zobisika za kumwamba ndi za dziko lapansi ndipo ndimadziwanso zonse zimene inu mumaulula ndi zimene mumabisa?”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قال ياآدم أنبئهم بأسمائهم فلما أنبأهم بأسمائهم قال ألم أقل لكم إني, باللغة نيانجا

﴿قال ياآدم أنبئهم بأسمائهم فلما أنبأهم بأسمائهم قال ألم أقل لكم إني﴾ [البَقَرَة: 33]

Khaled Ibrahim Betala
“(Allah) adanena: “E iwe Adam!: Auze mayina ake (azinthuzo).” Ndipo pamene adawauza mayina ake, (Iye) adati: “Kodi Sindinakuuzeni kuti Ine ndikudziwa zobisika zakumwamba ndi pansi, ndiponso ndikudziwa zimene mukuonetsera poyera ndi zimene mukubisa?”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek