×

Ndipo opani tsiku limene munthu sadzatha kuthandiza mnzake kapena kupepesa ndipo dipo 2:48 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:48) ayat 48 in Chichewa

2:48 Surah Al-Baqarah ayat 48 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 48 - البَقَرَة - Page - Juz 1

﴿وَٱتَّقُواْ يَوۡمٗا لَّا تَجۡزِي نَفۡسٌ عَن نَّفۡسٖ شَيۡـٔٗا وَلَا يُقۡبَلُ مِنۡهَا شَفَٰعَةٞ وَلَا يُؤۡخَذُ مِنۡهَا عَدۡلٞ وَلَا هُمۡ يُنصَرُونَ ﴾
[البَقَرَة: 48]

Ndipo opani tsiku limene munthu sadzatha kuthandiza mnzake kapena kupepesa ndipo dipo silidzalandiridwa ndiponso sadzathandizidwa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: واتقوا يوما لا تجزي نفس عن نفس شيئا ولا يقبل منها شفاعة, باللغة نيانجا

﴿واتقوا يوما لا تجزي نفس عن نفس شيئا ولا يقبل منها شفاعة﴾ [البَقَرَة: 48]

Khaled Ibrahim Betala
“Choncho opani tsiku lomwe munthu aliyense sadzathandiza mnzake ndi chilichonse, ndipo sikudzavomerezedwa kwa iye (munthuyo) dandaulo lililonse, ndiponso silidzalandiridwa dipo kwa iye; ndipo iwo sadzapulumutsidwa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek