×

Ndi mmene tidakupulumutsirani kwa anthu a Farawo, amene anali kukuzunzani kwambiri popha 2:49 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:49) ayat 49 in Chichewa

2:49 Surah Al-Baqarah ayat 49 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 49 - البَقَرَة - Page - Juz 1

﴿وَإِذۡ نَجَّيۡنَٰكُم مِّنۡ ءَالِ فِرۡعَوۡنَ يَسُومُونَكُمۡ سُوٓءَ ٱلۡعَذَابِ يُذَبِّحُونَ أَبۡنَآءَكُمۡ وَيَسۡتَحۡيُونَ نِسَآءَكُمۡۚ وَفِي ذَٰلِكُم بَلَآءٞ مِّن رَّبِّكُمۡ عَظِيمٞ ﴾
[البَقَرَة: 49]

Ndi mmene tidakupulumutsirani kwa anthu a Farawo, amene anali kukuzunzani kwambiri popha ana anu a amuna ndi kusiya ana anu a akazi. Ndithudi amenewa adali mayeso ochokera kwa Ambuye wanu

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وإذ نجيناكم من آل فرعون يسومونكم سوء العذاب يذبحون أبناءكم ويستحيون نساءكم, باللغة نيانجا

﴿وإذ نجيناكم من آل فرعون يسومونكم سوء العذاب يذبحون أبناءكم ويستحيون نساءكم﴾ [البَقَرَة: 49]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo (kumbukirani) pamene tidakupulumutsani kwa anthu a Farawo, omwe amakuzunzani ndi chilango choipa; adali kuzinga (kupha) ana anu achimuna ndikuwasiya moyo achikazi. Ndipo m’zimenezo mudali mayeso aakulu ochokera kwa Mbuye wanu
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek