Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 53 - البَقَرَة - Page - Juz 1
﴿وَإِذۡ ءَاتَيۡنَا مُوسَى ٱلۡكِتَٰبَ وَٱلۡفُرۡقَانَ لَعَلَّكُمۡ تَهۡتَدُونَ ﴾
[البَقَرَة: 53]
﴿وإذ آتينا موسى الكتاب والفرقان لعلكم تهتدون﴾ [البَقَرَة: 53]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo (kumbukiraninso) pamene Mûsa tidampatsa buku lolekanitsa choonadi ndi chonama kuti inu muongoke (polilingalira ndi kutsatira malamulo ake) |