Quran with Chichewa translation - Surah Ta-Ha ayat 111 - طه - Page - Juz 16
﴿۞ وَعَنَتِ ٱلۡوُجُوهُ لِلۡحَيِّ ٱلۡقَيُّومِۖ وَقَدۡ خَابَ مَنۡ حَمَلَ ظُلۡمٗا ﴾
[طه: 111]
﴿وعنت الوجوه للحي القيوم وقد خاب من حمل ظلما﴾ [طه: 111]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo nkhope (tsiku limenelo) zidzalobodoka pamaso pa (Allah) Wamoyo wamuyaya, Wochita chilichonse. Ndithu adzataika kwathunthu yense wochita zosalungama |