Quran with Chichewa translation - Surah Ta-Ha ayat 115 - طه - Page - Juz 16
﴿وَلَقَدۡ عَهِدۡنَآ إِلَىٰٓ ءَادَمَ مِن قَبۡلُ فَنَسِيَ وَلَمۡ نَجِدۡ لَهُۥ عَزۡمٗا ﴾
[طه: 115]
﴿ولقد عهدنا إلى آدم من قبل فنسي ولم نجد له عزما﴾ [طه: 115]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo tidamulangiza (Mneneri) Adam kale, koma adaiwala. Ndipo sitidapeze Mwa iye kulimba mtima (potsatira lamulo Lathu loti asadye zipatso za mtengo woletsedwa) |