Quran with Chichewa translation - Surah Ta-Ha ayat 50 - طه - Page - Juz 16
﴿قَالَ رَبُّنَا ٱلَّذِيٓ أَعۡطَىٰ كُلَّ شَيۡءٍ خَلۡقَهُۥ ثُمَّ هَدَىٰ ﴾
[طه: 50]
﴿قال ربنا الذي أعطى كل شيء خلقه ثم هدى﴾ [طه: 50]
Khaled Ibrahim Betala “(Mûsa) adati: “Mbuye wathu ndi yemwe adapatsa chinthu chilichonse chilengedwe chake, kenako adachiongolera (kutsata chimene chikulingana ndi chilengedwe chake).” |