Quran with Chichewa translation - Surah Ta-Ha ayat 69 - طه - Page - Juz 16
﴿وَأَلۡقِ مَا فِي يَمِينِكَ تَلۡقَفۡ مَا صَنَعُوٓاْۖ إِنَّمَا صَنَعُواْ كَيۡدُ سَٰحِرٖۖ وَلَا يُفۡلِحُ ٱلسَّاحِرُ حَيۡثُ أَتَىٰ ﴾
[طه: 69]
﴿وألق ما في يمينك تلقف ما صنعوا إنما صنعوا كيد ساحر ولا﴾ [طه: 69]
Khaled Ibrahim Betala ““Ndipo ponya chimene chili kudzanja lako ladzanjadzanja (ndodo); chimeza zomwe apanga; ndithu iwo apanga matsenga a mfiti ndipo mfiti siingapambane paliponse pamene yadza.” |