Quran with Chichewa translation - Surah Al-Anbiya’ ayat 25 - الأنبيَاء - Page - Juz 17
﴿وَمَآ أَرۡسَلۡنَا مِن قَبۡلِكَ مِن رَّسُولٍ إِلَّا نُوحِيٓ إِلَيۡهِ أَنَّهُۥ لَآ إِلَٰهَ إِلَّآ أَنَا۠ فَٱعۡبُدُونِ ﴾ 
[الأنبيَاء: 25]
﴿وما أرسلنا من قبلك من رسول إلا نوحي إليه أنه لا إله﴾ [الأنبيَاء: 25]
| Khaled Ibrahim Betala “Ndipo sitidatume patsogolo pako mtumiki aliyense koma tidali kumzindikiritsa kuti palibe mulungu wina wompembedza mwachoonadi, koma Ine; choncho ndilambireni |